Mateyu 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Mdyerekezi uja anamusiya+ ndipo kunabwera angelo nʼkuyamba kumutumikira.+