Mateyu 13:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena mʼnyumba mwake, koma kwina.”+ Luka 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ananena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, palibe mneneri amene amalandiridwa kwawo.+ Yohane 4:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Yesu mwiniwakeyo anachitira umboni kuti mneneri salemekezedwa kwawo.+
57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena mʼnyumba mwake, koma kwina.”+