-
Luka 13:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Yesu anayenda mumzinda ndi mzinda komanso mudzi ndi mudzi. Iye ankaphunzitsa nʼkumapitiriza ulendo wake wopita ku Yerusalemu.
-