Luka 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pambuyo pa zimenezi, Ambuye anasankha anthu ena 70 nʼkuwatumiza awiriawiri+ kuti atsogole kupita mumzinda ndi malo alionse kumene iye ankafunika kudzapitako.
10 Pambuyo pa zimenezi, Ambuye anasankha anthu ena 70 nʼkuwatumiza awiriawiri+ kuti atsogole kupita mumzinda ndi malo alionse kumene iye ankafunika kudzapitako.