Mateyu 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anayankha kuti: “Ena akumanena kuti ndinu Yohane Mʼbatizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumanena kuti Yeremiya kapena mmodzi wa aneneri.” Maliko 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anamuyankha kuti: “Akumanena kuti Yohane Mʼbatizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumanena kuti mmodzi wa aneneri.”
14 Iwo anayankha kuti: “Ena akumanena kuti ndinu Yohane Mʼbatizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumanena kuti Yeremiya kapena mmodzi wa aneneri.”
28 Iwo anamuyankha kuti: “Akumanena kuti Yohane Mʼbatizi,+ ena akumati Eliya,+ koma ena akumanena kuti mmodzi wa aneneri.”