Mateyu 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Senzani goli langa ndipo lolani kuti ndikuphunzitseni, chifukwa ndine wofatsa ndi wodzichepetsa+ ndipo mudzatsitsimulidwa. Mateyu 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yesu atamva zimenezi, anachoka kumeneko pangalawa nʼkupita kumalo kopanda anthu kuti akakhale payekha. Koma gulu la anthu litamva zimenezo, linamutsatira wapansi kuchokera mʼmizinda yawo.+
29 Senzani goli langa ndipo lolani kuti ndikuphunzitseni, chifukwa ndine wofatsa ndi wodzichepetsa+ ndipo mudzatsitsimulidwa.
13 Yesu atamva zimenezi, anachoka kumeneko pangalawa nʼkupita kumalo kopanda anthu kuti akakhale payekha. Koma gulu la anthu litamva zimenezo, linamutsatira wapansi kuchokera mʼmizinda yawo.+