Mateyu 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse nʼkukutsatirani, ndiye kodi tidzapeza chiyani?”+ Luka 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ngalawazo anafika nazo kumtunda, ndipo iwo anasiya chilichonse nʼkumutsatira.+
27 Kenako Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse nʼkukutsatirani, ndiye kodi tidzapeza chiyani?”+