Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+ Deuteronomo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani, kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali komanso kuti zinthu zikuyendereni bwino mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+ Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.”+ Limeneli ndi lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo. Lonjezo lake ndi lakuti:
12 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+
16 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani, kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali komanso kuti zinthu zikuyendereni bwino mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+
2 “Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu.”+ Limeneli ndi lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo. Lonjezo lake ndi lakuti: