Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 15:15-20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Petulo anamupempha kuti: “Timasulireni fanizo lija.” 16 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi inunso simunamvetse?+ 17 Kodi simukudziwa kuti chilichonse chimene chalowa mʼkamwa chimadutsa mʼmimba ndipo chimakatayidwa kuchimbudzi? 18 Koma chilichonse chimene chimatuluka pakamwa chimachokera mumtima ndipo zinthu zimenezo ndi zimene zimaipitsa munthu.+ 19 Mwachitsanzo, mumtima mumachokera maganizo oipa awa:+ maganizo a kupha anthu, a chigololo, a chiwerewere,* a kuba, maumboni onama komanso kunyoza Mulungu. 20 Zimenezi ndi zinthu zimene zimaipitsa munthu, koma kudya chakudya osasamba mʼmanja* sikuipitsa munthu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena