Maliko 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anagwira dzanja la munthu wosaonayo nʼkupita naye kunja kwa mudzi. Kumeneko iye anaika malovu mʼmaso mwa munthuyo+ nʼkuika manja ake pa munthuyo ndipo anamufunsa kuti: “Kodi ukuona chilichonse?” Yohane 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atanena zimenezi, analavulira malovu pansi nʼkukanda matope ndi malovuwo, kenako anapaka matopewo mʼmaso mwa munthuyo.+
23 Iye anagwira dzanja la munthu wosaonayo nʼkupita naye kunja kwa mudzi. Kumeneko iye anaika malovu mʼmaso mwa munthuyo+ nʼkuika manja ake pa munthuyo ndipo anamufunsa kuti: “Kodi ukuona chilichonse?”
6 Atanena zimenezi, analavulira malovu pansi nʼkukanda matope ndi malovuwo, kenako anapaka matopewo mʼmaso mwa munthuyo.+