Mateyu 7:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu atamaliza kulankhula mawu amenewa, gulu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa ndi kaphunzitsidwe kake,+ 29 chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu waulamuliro,+ osati ngati alembi awo.
28 Yesu atamaliza kulankhula mawu amenewa, gulu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa ndi kaphunzitsidwe kake,+ 29 chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu waulamuliro,+ osati ngati alembi awo.