Mateyu 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno alembi ndi Afarisi ena anamupempha kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutionetse chizindikiro.”+ Yohane 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro chotani+ kuti ife tichione nʼkukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?
30 Ndiyeno iwo anamufunsa kuti: “Ndiye inuyo muchita chizindikiro chotani+ kuti ife tichione nʼkukukhulupirirani? Muchita ntchito yotani?