Maliko 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iye anawafunsa kuti: “Muli ndi mitanda ingati ya mkate? Pitani mukaone!” Ataiona ananena kuti: “Ilipo 5 ndi nsomba ziwiri.”+
38 Iye anawafunsa kuti: “Muli ndi mitanda ingati ya mkate? Pitani mukaone!” Ataiona ananena kuti: “Ilipo 5 ndi nsomba ziwiri.”+