Mateyu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake?+ Kapena kodi munthu angapereke chiyani choti asinthanitse ndi moyo wake?+ Luka 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake kapena kudzivulaza?+
26 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake?+ Kapena kodi munthu angapereke chiyani choti asinthanitse ndi moyo wake?+
25 Kodi munthu angapindule chiyani ngati atapeza zinthu zonse zamʼdzikoli koma nʼkutaya moyo wake kapena kudzivulaza?+