Mateyu 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa mʼpangʼono pomwe mpaka choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga Mfumu.”+ Luka 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma ndithu ndikukuuzani, pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa mʼpangʼono pomwe mpaka choyamba ataona Ufumu wa Mulungu.”+
28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa mʼpangʼono pomwe mpaka choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga Mfumu.”+
27 Koma ndithu ndikukuuzani, pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa mʼpangʼono pomwe mpaka choyamba ataona Ufumu wa Mulungu.”+