Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 8:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano Yesu, atalowa mʼnyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali chigonere, akudwala malungo.*+ 15 Choncho anagwira dzanja la mayiwo+ ndipo malungowo anatheratu, moti anadzuka nʼkuyamba kumutumikira.

  • Luka 4:38, 39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Atatuluka mʼsunagogemo, anakalowa mʼnyumba ya Simoni. Pa nthawiyo apongozi aakazi a Simoni ankadwala malungo aakulu,* choncho anamupempha kuti awathandize.+ 39 Ndiyeno anaima pamene mayiwo anagona nʼkuwachiritsa ndipo malungowo anatheratu. Nthawi yomweyo mayiwo anadzuka nʼkuyamba kuwatumikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena