Luka 9:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kenako Yohane ananena kuti: “Mlangizi, ife tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiye tinamuletsa, chifukwa sakuyenda ndi ife.”+
49 Kenako Yohane ananena kuti: “Mlangizi, ife tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiye tinamuletsa, chifukwa sakuyenda ndi ife.”+