Mateyu 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso ngati dzanja lako lamanja limakuchimwitsa, ulidule nʼkulitaya.+ Chifukwa ndi bwino kuti ukhale wopanda chiwalo chimodzi kusiyana ndi kuti thupi lako lonse lidzaponyedwe mʼGehena.*+ Mateyu 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule nʼkulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana nʼkuti uponyedwe mʼmoto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+ Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi lanu+ padziko lapansi kukhala zakufa ku chiwerewere,* zinthu zodetsa, chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ kulakalaka zinthu zoipa komanso dyera limene ndi kulambira mafano.
30 Komanso ngati dzanja lako lamanja limakuchimwitsa, ulidule nʼkulitaya.+ Chifukwa ndi bwino kuti ukhale wopanda chiwalo chimodzi kusiyana ndi kuti thupi lako lonse lidzaponyedwe mʼGehena.*+
8 Choncho ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule nʼkulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana nʼkuti uponyedwe mʼmoto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi lanu+ padziko lapansi kukhala zakufa ku chiwerewere,* zinthu zodetsa, chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ kulakalaka zinthu zoipa komanso dyera limene ndi kulambira mafano.