Luka 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma tsiku limene Loti anatuluka mu Sodomu, kumwamba kunagwa moto ndi sulufule ngati mvula nʼkuwononga anthu onse.+
29 Koma tsiku limene Loti anatuluka mu Sodomu, kumwamba kunagwa moto ndi sulufule ngati mvula nʼkuwononga anthu onse.+