Akolose 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi zonse mawu anu azisonyeza kuti ndinu okoma mtima ndipo azikhala okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire munthu aliyense.+
6 Nthawi zonse mawu anu azisonyeza kuti ndinu okoma mtima ndipo azikhala okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire munthu aliyense.+