Aroma 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati nʼkotheka, yesetsani mmene mungathere kuti muzikhala mwamtendere ndi anthu onse.+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu owola asamatuluke pakamwa panu,+ koma pazituluka mawu abwino okha kuti alimbikitse ena pakafunika kutero, kuti athandize anthu amene akumvetsera.+ 1 Atesalonika 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+ Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.
29 Mawu owola asamatuluke pakamwa panu,+ koma pazituluka mawu abwino okha kuti alimbikitse ena pakafunika kutero, kuti athandize anthu amene akumvetsera.+
13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+
14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.