Mateyu 3:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho anthu ochokera ku Yerusalemu ndi mʼchigawo chonse cha Yudeya ndiponso ochokera mʼmidzi yonse yapafupi ndi Yorodano ankapita kwa iye.+ 6 Iye ankawabatiza* mumtsinje wa Yorodano+ ndipo anthuwo ankaulula machimo awo poyera.
5 Choncho anthu ochokera ku Yerusalemu ndi mʼchigawo chonse cha Yudeya ndiponso ochokera mʼmidzi yonse yapafupi ndi Yorodano ankapita kwa iye.+ 6 Iye ankawabatiza* mumtsinje wa Yorodano+ ndipo anthuwo ankaulula machimo awo poyera.