Deuteronomo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho mudziwe kuti Yehova Mulungu wanu sakukupatsani dziko labwinoli chifukwa choti ndinu olungama, paja ndinu anthu ouma khosi.+ Machitidwe 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa zaka pafupifupi 40, iye anapirira khalidwe lawo mʼchipululu.+
6 Choncho mudziwe kuti Yehova Mulungu wanu sakukupatsani dziko labwinoli chifukwa choti ndinu olungama, paja ndinu anthu ouma khosi.+