Genesis 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa cha zimenezi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake nʼkudziphatika kwa mkazi wake* ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+ Aefeso 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Chifukwa cha zimenezi mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake nʼkudziphatika kwa* mkazi wake ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi.”+
24 Chifukwa cha zimenezi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake nʼkudziphatika kwa mkazi wake* ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+
31 “Chifukwa cha zimenezi mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake nʼkudziphatika kwa* mkazi wake ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi.”+