Ekisodo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musaphe munthu.*+ Deuteronomo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musaphe munthu.*+ Mateyu 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti: ‘Musaphe munthu.+ Aliyense amene wapha munthu wapalamula mlandu wa kukhoti.’+ 1 Yohane 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene amadana ndi mʼbale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu sadzalandira moyo wosatha.+
21 Inu munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti: ‘Musaphe munthu.+ Aliyense amene wapha munthu wapalamula mlandu wa kukhoti.’+
15 Aliyense amene amadana ndi mʼbale wake ndi wopha munthu,+ ndipo mukudziwa kuti aliyense wopha munthu sadzalandira moyo wosatha.+