Mateyu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno mayi wina amene ankadwala matenda otaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake nʼkugwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ Mateyu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anatembenuka ndipo anaona mayiyo nʼkunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+
20 Ndiyeno mayi wina amene ankadwala matenda otaya magazi kwa zaka 12+ anafika kumbuyo kwake nʼkugwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+
22 Yesu anatembenuka ndipo anaona mayiyo nʼkunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+