Luka 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mbiri yake inafalikira kwambiri ndipo magulu a anthu ankasonkhana pamodzi kudzamumvetsera komanso kudzachiritsidwa matenda awo.+
15 Koma mbiri yake inafalikira kwambiri ndipo magulu a anthu ankasonkhana pamodzi kudzamumvetsera komanso kudzachiritsidwa matenda awo.+