Mateyu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yohane ankavala chovala chaubweya wa ngamila ndi lamba wachikopa mʼchiuno mwake.+ Chakudya chake chinali dzombe ndi uchi.+
4 Yohane ankavala chovala chaubweya wa ngamila ndi lamba wachikopa mʼchiuno mwake.+ Chakudya chake chinali dzombe ndi uchi.+