Mateyu 27:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno achifwamba awiri anapachikidwa naye limodzi. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja ndipo wina anali kumanzere kwake.+
38 Ndiyeno achifwamba awiri anapachikidwa naye limodzi. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja ndipo wina anali kumanzere kwake.+