Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+ Salimo 109:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iwo akumandinyoza.+ Akandiona akumapukusa mitu yawo.+ Yesaya 53:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu ankamupewa,+Anali munthu amene kupweteka ankakudziwa bwino* ndipo matenda ankawadziwa. Zinali ngati kuti nkhope yake yabisika kwa ife.* Ananyozedwa ndipo tinkamuona ngati wopanda pake.+
7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+
3 Iye ananyozedwa ndipo anthu ankamupewa,+Anali munthu amene kupweteka ankakudziwa bwino* ndipo matenda ankawadziwa. Zinali ngati kuti nkhope yake yabisika kwa ife.* Ananyozedwa ndipo tinkamuona ngati wopanda pake.+