Mateyu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼbadwo woipa komanso wachigololo* ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena zimenezi, anachoka nʼkuwasiya.
4 Mʼbadwo woipa komanso wachigololo* ukufunitsitsabe chizindikiro, koma sudzapatsidwa chizindikiro chilichonse+ kupatulapo chizindikiro cha Yona chokha.”+ Atanena zimenezi, anachoka nʼkuwasiya.