Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoweli 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Zimenezi zikadzachitika ndidzapereka* mzimu wanga+ kwa chamoyo chilichonse,

      Ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzalosera.

      Amuna achikulire adzalota maloto,

      Ndipo anyamata adzaona masomphenya.+

  • Machitidwe 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano onse anali atasonkhana pamodzi pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite.+

  • Machitidwe 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+

  • Machitidwe 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zitatero ndinakumbukira mawu amene Ambuye ankakonda kunena aja akuti, ‘Yohane ankabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+

  • 1 Akorinto 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena