Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 42:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza,

      Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+

      Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+

      Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+

  • Mateyu 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka mʼmadzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda nʼkudzamutera.+

  • Yohane 1:32-34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Yohane anachitiranso umboni kuti: “Ndinaona mzimu ukutsika ngati nkhunda kuchokera kumwamba ndipo unakhalabe pa iye.+ 33 Inenso sindinkamudziwa, koma Mulungu amene anandituma kudzabatiza mʼmadzi anandiuza kuti: ‘Ukadzaona mzimu ukutsika nʼkukhazikika pamunthu wina,+ ameneyo ndi amene amabatiza ndi mzimu woyera.’+ 34 Ine ndinaonadi zimenezo ndipo ndachitira umboni kuti iyeyu ndi Mwana wa Mulungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena