Luka 1:59, 60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pa tsiku la 8, iwo anabwera kudzachita mdulidwe wa mwanayo+ komanso ankafuna kumupatsa dzina la bambo ake, lakuti Zekariya. 60 Koma mayi ake anayankha kuti: “Limenelo ayi! Dzina lake akhala Yohane.”
59 Pa tsiku la 8, iwo anabwera kudzachita mdulidwe wa mwanayo+ komanso ankafuna kumupatsa dzina la bambo ake, lakuti Zekariya. 60 Koma mayi ake anayankha kuti: “Limenelo ayi! Dzina lake akhala Yohane.”