Mateyu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawiyo Herode, wolamulira chigawo,* anamva za Yesu+ Luka 23:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atamva zimenezo, Pilato anafunsa ngati munthuyu ndi Mgalileya. 7 Ndiyeno atadziwa kuti akuchokera mʼchigawo chimene amalamulira Herode,+ anamutumiza kwa Herode, amenenso mʼmasiku amenewo anali mu Yerusalemu.
6 Atamva zimenezo, Pilato anafunsa ngati munthuyu ndi Mgalileya. 7 Ndiyeno atadziwa kuti akuchokera mʼchigawo chimene amalamulira Herode,+ anamutumiza kwa Herode, amenenso mʼmasiku amenewo anali mu Yerusalemu.