-
Luka 1:80Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
80 Choncho mwana uja anakula ndipo analimba mwauzimu. Iye anapitiriza kukhala mʼchipululu mpaka tsiku limene anadzionetsera poyera kwa Isiraeli.
-