Mateyu 3:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼmasiku amenewo, Yohane+ Mʼbatizi anapita mʼchipululu cha Yudeya nʼkuyamba kulalikira.+ 2 Iye ankalalikira kuti: “Lapani, chifukwa Ufumu wakumwamba wayandikira.”+ Maliko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yohane Mʼbatizi anali mʼchipululu ndipo ankalalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Luka 1:76, 77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 76 Koma kunena za mwana wamngʼonowe, udzatchedwa mneneri wa Wamʼmwambamwamba, chifukwa udzatsogola pamaso pa Yehova* kuti ukakonze njira zake.+ 77 Kuti ukathandize anthu ake kudziwa za chipulumutso chimene chidzatheke machimo awo akadzakhululukidwa,+
3 Mʼmasiku amenewo, Yohane+ Mʼbatizi anapita mʼchipululu cha Yudeya nʼkuyamba kulalikira.+ 2 Iye ankalalikira kuti: “Lapani, chifukwa Ufumu wakumwamba wayandikira.”+
4 Yohane Mʼbatizi anali mʼchipululu ndipo ankalalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+
76 Koma kunena za mwana wamngʼonowe, udzatchedwa mneneri wa Wamʼmwambamwamba, chifukwa udzatsogola pamaso pa Yehova* kuti ukakonze njira zake.+ 77 Kuti ukathandize anthu ake kudziwa za chipulumutso chimene chidzatheke machimo awo akadzakhululukidwa,+