Luka 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Zakeyu anaimirira nʼkuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense* ndibweza kuwirikiza ka 4.”+
8 Koma Zakeyu anaimirira nʼkuuza Ambuye kuti: “Ambuye, ine ndipereka ndithu hafu ya chuma changa kwa osauka. Ndipo chilichonse chimene ndinalanda munthu aliyense* ndibweza kuwirikiza ka 4.”+