Ekisodo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Musafalitse nkhani yabodza.+ Musamagwirizane ndi munthu woipa pokhala mboni yokonzera wina zoipa.+ Ekisodo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musamagwirizane ndi anthu amene akuneneza munthu mlandu wabodza.* Musamaphe munthu wosalakwa komanso wolungama, chifukwa woipa sindidzamuona kuti ndi wolungama.*+ Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musamabe,+ musamapusitse anzanu+ ndiponso musamachitirane chinyengo.
23 “Musafalitse nkhani yabodza.+ Musamagwirizane ndi munthu woipa pokhala mboni yokonzera wina zoipa.+
7 Musamagwirizane ndi anthu amene akuneneza munthu mlandu wabodza.* Musamaphe munthu wosalakwa komanso wolungama, chifukwa woipa sindidzamuona kuti ndi wolungama.*+