-
Yohane 1:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho anamufunsa kuti: “Nanga nʼchifukwa chiyani umabatiza anthu ngati iweyo si iwe Khristu, Eliya kapena Mneneri?”
-