Yohane 1:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yohane anawayankha kuti: “Ine ndimabatiza mʼmadzi. Pakati panu paimirira wina amene inu simukumudziwa. 27 Iye ndi amene akubwera mʼmbuyo mwangamu ndipo ine si woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.”+
26 Yohane anawayankha kuti: “Ine ndimabatiza mʼmadzi. Pakati panu paimirira wina amene inu simukumudziwa. 27 Iye ndi amene akubwera mʼmbuyo mwangamu ndipo ine si woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.”+