2 Samueli 5:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide atachoka ku Heburoni nʼkupita ku Yerusalemu anakwatiranso akazi ena komanso anali ndi akazi apambali+ ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.+ 14 Ana amene Davide anabereka ku Yerusalemu ndi awa: Samuwa, Sobabu, Natani,+ Solomo,+ 1 Mbiri 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya, Sobabu, Natani+ ndi Solomo.+ Ana 4 amenewa mayi awo anali Bati-seba+ mwana wa Amiyeli.
13 Davide atachoka ku Heburoni nʼkupita ku Yerusalemu anakwatiranso akazi ena komanso anali ndi akazi apambali+ ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.+ 14 Ana amene Davide anabereka ku Yerusalemu ndi awa: Samuwa, Sobabu, Natani,+ Solomo,+
5 Ku Yerusalemu+ iye anabereka ana awa: Simeya, Sobabu, Natani+ ndi Solomo.+ Ana 4 amenewa mayi awo anali Bati-seba+ mwana wa Amiyeli.