-
Rute 4:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho Boazi anatenga Rute kukhala mkazi wake ndipo anagona naye. Yehova anamudalitsa ndipo anatenga pakati nʼkubereka mwana wamwamuna.
-