Rute 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi,+ amene Tamara anaberekera Yuda.” Rute 4:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mzere wa ana a Perezi+ unayenda chonchi: Perezi anabereka Hezironi,+ 19 Hezironi anabereka Ramu, Ramu anabereka Aminadabu,+ 1 Mbiri 2:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara,+ mpongozi wake, anamʼberekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda analipo 5. 5 Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+
12 Ndipo kudzera mwa ana amene Yehova adzakupatsa kwa mtsikanayu,+ nyumba yako ikhale ngati nyumba ya Perezi,+ amene Tamara anaberekera Yuda.”
18 Mzere wa ana a Perezi+ unayenda chonchi: Perezi anabereka Hezironi,+ 19 Hezironi anabereka Ramu, Ramu anabereka Aminadabu,+
4 Tamara,+ mpongozi wake, anamʼberekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda analipo 5. 5 Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+