Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pake, mʼbale wake anabadwa, ndipo dzanja lake linali litagwira chidendene cha Esau.+ Choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.*+ Pamene Rabeka ankabereka anawa nʼkuti Isaki ali ndi zaka 60.
26 Pambuyo pake, mʼbale wake anabadwa, ndipo dzanja lake linali litagwira chidendene cha Esau.+ Choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.*+ Pamene Rabeka ankabereka anawa nʼkuti Isaki ali ndi zaka 60.