Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ Deuteronomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Muziopa Yehova Mulungu wanu+ nʼkumamutumikira,+ ndipo muzilumbira pa dzina lake.+ Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova Mulungu wanu muzimuopa, muzimutumikira,+ muzikhala naye pafupi kwambiri komanso muzilumbira pa dzina lake.
20 Yehova Mulungu wanu muzimuopa, muzimutumikira,+ muzikhala naye pafupi kwambiri komanso muzilumbira pa dzina lake.