Mateyu 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu atamaliza kulankhula mawu amenewa, gulu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa ndi kaphunzitsidwe kake,+ Yohane 7:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Alondawo anayankha kuti: “Palibe munthu amene analankhulapo ngati iyeyu nʼkale lonse.”+
28 Yesu atamaliza kulankhula mawu amenewa, gulu la anthulo linakhudzidwa moti linadabwa ndi kaphunzitsidwe kake,+