Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 8:28, 29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Atafika kutsidya linalo, mʼdera la Agadara, anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda akuchokera mʼmanda.*+ Amunawa anali ochititsa mantha kwambiri moti panalibe aliyense amene ankalimba mtima kudutsa msewu umenewo. 29 Nthawi yomweyo iwo anafuula kuti: “Kodi mukufuna chiyani kwa ife, Mwana wa Mulungu?+ Kodi mwabwera kudzatipatsa chilango+ nthawi yoikidwiratu isanakwane?”+

  • Maliko 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ngakhalenso mizimu yonyansa,+ inkati ikamuona, inkadzigwetsa pansi pamaso pake nʼkufuula kuti: “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena