Aheberi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndiye tidzapulumuka bwanji ngati titanyalanyaza chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutsochi+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.
3 ndiye tidzapulumuka bwanji ngati titanyalanyaza chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutsochi+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.