Maliko 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Nʼchifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyozatu Mulungu ameneyu. Ndi ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha basi?”+ Luka 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa kuti: “Kodi ameneyu ndi ndani kuti azinyoza Mulungu chonchi? Winanso ndi ndani amene angakhululukire machimo kupatulapo Mulungu?”+
7 “Nʼchifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyozatu Mulungu ameneyu. Ndi ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha basi?”+
21 Kenako alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa kuti: “Kodi ameneyu ndi ndani kuti azinyoza Mulungu chonchi? Winanso ndi ndani amene angakhululukire machimo kupatulapo Mulungu?”+